
Makhonsolo bwezani K1.3 billion yathu yomwe mukulephera kuyifotokozera – yatero World Bank
Advertisement Banki yayikulu pa dziko lonse – World Bank yalamula ma khonsolo mdziko muno kuti abweze ndalama zokwana 1.3 billion Kwacha za mndondomeko yothandizira kutukula miyoyo ya anthu pansi pa Social Support for Resilient Livelihood Project (SSRLP), …